Anda di halaman 1dari 5

6DPSOH&KLFKHZDVHQWHQFHV

Caveat: These sample Chichewa sentences were compiled by a beginning student of Chichewa
based on class notes, and thus it is not particularly well organized nor guaranteed for accuracy;
2) This list may be downloaded from http://nature.berkeley.edu/~alyons/chichewa/.

WEEK 1
Bambo Andy a ma chokera ku Florida. Mr. Andy is from Florida.
Mu ma pita kuti? Where do you go (habitually)?
Mu ku funa chiyani? What do you want?
A na nena kuti... He said that...
Mu ku funa chiyani? What do you want?
Ti dza phunzira. We will learn.
Ana a ma konda mitengo. Children love trees.
Mkango u ma thawa mitengo The lion runs away from the trees.
Mipando i ma gwa. Chairs fall.
Ana anga a ma phunzira chingerezi. My children learn English.
Mkango wanga (u+anga - anga starts with a My lion is learning.
vowel) u ku phunzira.
Mikango yanga (i+anga) i ku phunzira. My lions are learning.
Kamkango kanga ka li bwino. My small lion in ok.
Msika u li pafudi ndi downtown. There is a market near downtown.
Kodi ku li msika? Is there a market?
Mikango i ma dya anthu. Lions eat people.
Mpanda wa mphunzitsi. The teacher’s chair.
Muwa gula chiyani? What have you just bought?
Mu a dya chiyani? What did you just eat?
Ndi ku topa. I am getting tired.
Nda topa. (ndi+a) I am tired.
Nda kondwa. I am happy.
Ana a topa. The children are tired.
Ife ti ma phunzira ku California. We learn in California.
Ndi a chokera. I am just from.
Ndi ma chokera. I am from (originally)
Nda chedwa. I am late.
Mu ku chedwa. I am running late.
Mwa chedwa. You are late.
Uyu mayi This woman
Dzina langa ndi Andy. My name is Andy.
Dzina lake ndani? What is his name?
Mkango uku werenga. The lion is reading.
Funso langa li ku nena kuti My question says that
Mikango iku thawa munthu The lion runs away from people.
Mkono wanga uku lemba. My arm is writing.
Mikono yanga iku lemba. My arms are writing.

1
Kamkango kama kanda mtengo. The little lion scratches the tree.
Mphunzitsi a ku lota The teachers are dreaming.
Mikango ya (i-a) mfumu i ku lota. The chief’s lions are dreaming.
Kodi mu ma mwa mowa? Do you drink beer?
Mayi uyu a ku nena kuti... This woman is saying...
Mayankho aanu Our responses
Ana aanu a li ndi nsabwe. Your children have lice.
Mwana wanu (u+anu) a li ndi nsabwe. Your child has lice.
Ku li mapiri. There are mountains.
Mapiri athu a li ndi njovu. Our mountains have elephants.
Funso lanu li li ndi bodza. Your question has lies.
Khomo li li ndi chutseko. The entrance has a door.
Mphunzitsa a ku gula mkango The teacher is buying a lion.
Mphunzitsa a ku u gula. The teacher is buying it (class 3 noun - lion)
Mphunzitsa a ku li gula The teacher is buying it (class 5 noun)
Ndi ku thamangitsa mkango. I am chasing the lion.
Ndi ku u thamangitsa. I am chasing it (class 3 noun - lion)
U ku ndi thamangitsa. It (class 3 noun) is chasing me.
Mkono wanu (u-anu) u li ndi chiyani? Your arm has what?
Ndi li ndi ludzu. I am thirsty.
Ndi li ndi njaba. I am hungry.
Chipatala chanthu chi li ndi ziseko. Our hospital has doors.

WEEK 2
Mikango ya (i-a) ku LA si (si-i-ma) bangula, Lions from LA don’t roar, but they of Ohio do
koma ya ku Ohio i ma bangula. roar.
Ku Irvine kulibe wildlife. At Irvine there is no wildlife.
Inu bambo... You sir... (emphatic)
Nda pita I am about to go. (I’m off).
Mu dya chiyani? What will you eat for lunch (soon)?
We shall see each other soon. Tionana posachedwa.
Tamva (ti-a-mva) We have heard.
Ku Maryland ku libe mikango. Ku VA ku In Maryland there are no lions. In Virginia
libenso mikango. there are also no lions.
Ndi libe assignment yanga (i-anga) chifukwa I do not have my assignment because I do not
ndi libe printer. have a printer.
Ndi na funsa bambo Ken kuti... I asked Mr. Ken that....
Ndi na u thamangitsa. I chased it.
U na ndi thamangitsa. It chased me.
A ku funa ku ti phunzitsa. He wants to teach us.
Ndi ku funa kuti mu sambire. I want that you swim.
Muyende bwino. Travel well.
Mu nenenso. Say it again.
Si ndi kumva. I don’t hear (understand).
Mu nenenso pang’ono pang’ono. Say it again slowly.

2
Ti pite ku kalasi tsopano. Let’s go to class now.
Mu na samukira liti ku Santa Cruz? When did you move to Santa Cruz?
Ndi ku funa kuti mu ndi yahkhe. I want you to answer me.
A (a-a) ndi yankha chiyani? He responded to me what?
A (a-a) ku-yankha-ni kuti a na samukira ku He responded to you that he moved to Santa
Santa Cruz chaka cha 1985. Cruz in 1985.
Si a ku khala ku Ohio. He isn’t living in Ohio.
Mu a ti uza... You have told us...
Ndi ku funa kuti mu ndi uze I want you to tell us...
Ti a tsiriza phunziro lathu la Chichewa. We have finished our lesson of Chichewa.
A dza tsiriza liti? When will she finish?
Ndi ku ka gula chakudya. I am going (somewhere) to buy food.
Mu ku ka chita chiyani? You are going (somewhere) to do what?
Ndi ku pita ku San Fransisco ku ka gulitsa I am going to San Fransisco to sell my books.
mabuku anga (a-anga).
Mu ku dza chita chiyani? You are coming (here) to do what?
Ti ku funa kuti mu ka chotse njoka yanu (i- We want you to go (there) remove your snake.
anu).
Pitani mu ka i chotse. Go remove it (snake class 9).
Mu ku gula chiyani? You are buying what?
Mu ku ka gula chiyani? You are going (somewhere) to buy what?
Mu ku dza gula chiyani? You are coming (here) to buy what?
Mu dza gula chiyani? You will buy what?
Mu gula chiyani? You will (soon) buy what?
Mu ka gula chiyani? You will (soon) go to buy what?
Ndi ku ka zi gulitsa ku San Fransisco. I am going to sell them (snakes, class 10) in
San Fransisco.
Si ndi ku nena kuti mu gulitse. I am not saying that you sell them.
Ndi ku nena kuti mu sa gulitse. I am saying that you not sell them.
Mu sa (sa-a) mvere. Don’t listen to him.
Mu sa (sa-a) lembe. Don’t write it.
Iyayi, ndi libe funsa. No, I don’t have a question.
Ndi ma ku-konda-ni. I love you.
Dzina la nanga ndi chiyani? Name of lake is what?
A ø ku-sokoneza-ni. He will confuse you.
Ndi ku funa kwambiri... I like very much....
I don’t know. Si ndi ku dziwa.
Mountains are in West Texas. Maphiri a li ku West Texas.
Mu sa dandaule. Don’t worry.
Mu ø ka pume. You go (somewhere) rest.
U na tha liti? It (meeting class 3) ended when?
Galimoto yanga ndi ya mtundu wa Ford. My car is of type of Ford.
Mu ti uze. You tell us.
Bambo Ken a nena kuti a li ndi jeep. Bambo Ken (just) told us that he has a jeep.
Sa (si-a) khala ku VA. Hi is not from Virginia (ma omitted)

3
Week 3
Ndi ku li dziwa. I know it.
Ti li ndi muthu modzi (m-modzi) We have one person
Chipatala chimenu chili ndi mankhwala The hospital with a lot of medicne receives....
ambiri chima lundira....
State ya Ohio ili ku dera liti la Amerika? State of Ohio is is which region of Amerika?
Anthu a ku TX a ma weta njoka zanji (zi- People of Texas raise which snakes?
anji)?
Chibali ndi fupa, si chi ma ola Brotherhood is bones. It does not rot. (proverb)
Tiyende pamodzi ndi mtima umodzi. Let’s walk together with one heart.

Week 4
Kuyendetsa galimoto ku ma ndi vuta. Driving car is giving me problem.
Abale a ma vuta. Relatives cause problems.
Ndi li ndi vuto. I have problem.
Ndi li m’mavuto. I am in problems (trouble).
Ndi li pa mavuto. I am in/at problems.
Sabata yatha (i-a-tha). Last week.
Ndi na pita ku ka sambire. I went to go swim.
Si mu na ka sambire ku Santa Monica. I didn’t go swim at Santa Monica.
Museum i-mene munapita ku-ka-i-ona ili The museum which you went to go see (it) is
kuti? where?
Mbudzi zimene Mayi Jacqui a-ma-zi-weta zi- Goats which Mayi Jacqui herds (them) are in
li ku dambo. the swamp.
Anyamata amene tinawaona ku nyanja... The boys which we saw (them) at the lake...
Ku na li chiyani? There was what?
Ulendo wa bwino, koma tayenda (ti-a-yenda) Good journey, but we traveled on foot.
pansi.
Mzinda wa Santa Cruz uli ku mpoto ku a City of Santa Cruz is at north at California.
California.
Ndi na ku-phunzitsa-ni. I taught you.
Mutsogole. You go ahead.
Ndi li pa mnyenyo. I am on break.
Ti yambanso. We will (shortly) begin again.
Tinadya nyama ndi kumwa mowa ndi kuotcha We ate meat and drank beer and roasted (on
msomba. open fire) fish.
Ndi na bwerako dzulo madzulo. I returned yesterday night.
A na pita pa galimoto. He went on (by) car.
Ndi yani? With who?
Ndi ndani? With who?
Ku Chicago ku ma zizira. Chicago gets cold.
Ku California ku ku tentha. At California is getting hot.
Ku California ku ma tentha. At California is (habitually) hot.
Mpando wanga uku wawa. My arm is hurting.

4
Mu ma tha...? Can you....?
Nda (ndi-a) tha. I am finished.
Tsopano ndi vuto lanu. Now it’s your problem.
Mu a ti uza (zinthu omitted) zimene Bambo You have told us the (things) which Andy has
Andy anandiyankha. answered me.
Ndikufuna ku ku-funsa-ni. I want to ask you.
Mu ma chi (chilankhulo) phunzitsi kuti? You have learned it (language) where?
Kucheza kuathu ku ku khudza... Our chatting is touching upon...
Kodi nkhani yanu i-ku-khudza chiyani. Your news is touching (concerning) what?
Dziko la Mexico li li kumwera ku-a Amerika. Country of Mexico is south of America.
A ma chita research. He does research.
Pang’ono pang’ono ndi mtolo. Slowly is a bundle. Meaning: what you gather
in small quantities adds up to a big bundle.
Tsokonombwe anatha mtunda ndi kulumpha. Insect finishes (covers) land with jumps.
Meaning: tackle a big job in small bits.
Mfiti si-i lumpha maliro. Someone who practices witchcraft doesn’t
jump (miss) funerals. Meaning: don’t miss
opportunities that interest you.
Si ndi nga ku-uze-ni. I can not tell you.
Si ndi ma ku-uza-ni zimene ndimachita usiku. I do not tell you (things) which I do at night.
Mkango u ku thamangitsa mbuzi. Lion is chasing the goats.
U-na-li ndi yani? You (familiar - because speaker is angry) were
with who?
Mu li ndi nsanje. You have jealousy.
Mu ku chita nsanje. You are jealousy.
Chidindo cha jombo chi-a-bwera bwanji, The stamp of a print came how into my house?
mnyumba mwanga?
Nda chita mwawi. I am doing lucky (you are lucky).
Mu li ndi mwawi. You have luck.
A ku chita manyazi. She is shy.
Ndi li ndi tsoka. I have bad luck.
Tsoka langa. Just my luck (lit. my bad luck)
Zinthu za (zi-a) tsopano. New things (lit. things of now.)
Nzeru za kale. Ancient wisdom (lit intelligence of old)
Tingathe ku-mu-yankha. We are able to answer him.
Mu khoza ku ka dya. You are able to go eat.

Anda mungkin juga menyukai